A A A A A


Sakani

MATEYU 6:9
Cifukwa cace pempherani inu comweci: Atate wathu wa Kumwamba, Dzina lanu liyeretsedwe.


MATEYU 9:38
Cifukwa cace pempherani Mwini zotuta kuti akokose anchito kukututakwace.


MATEYU 24:20
Ndipo pempherani kuti kuthawa kwanu kusakhale pa nyengo yacisanu, kapena pa Sabata;


Mark 13:18
Ndipo pempherani kuti kusakhale m'nyengo yacisanu.


Mark 13:33
Yang'anirani, dikirani, pempherani: pakuti simudziwa nthawi yace.


Mark 14:38
Dikirani, pempherani, kuti mungalowe m'kuyesedwa; mzimutu uli wakufuna, koma thupi liri lolefuka.


1 ATESALONIKA 5:17
Pempherani kosaleka;


Chewa Bible (BL) 1992
Zambia Bible Society, Malawi Bible Society and Zimbabwe Bible Society