1 |
Buku lofotokoza za mʼbado wa Yesu Khristu mwana wa Davide, mwana wa Abrahamu: |
2 |
Abrahamu anabereka Isake, Isake anabereka Yakobo, Yakobo anabereka Yuda ndi abale ake. |
3 |
Yuda anabereka Perezi ndi Zara, amene amayi awo anali Tamara. Perezi anabereka Hezironi, Hezironi anabereka Aramu. |
Chewa Bible 2016 |
|
1 |
Buku la kubadwa kwa Yesu Khristu, mwana wa Davide, mwana wa Abrahamu. |
2 |
Abrahamu anabala Isaki; ndi Isaki anabala Yakobo; ndi Yakobo anabala Yuda ndi abale ake; |
3 |
ndi Yuda anabala Perezi ndi Zera mwa Tamara; ndi Perezi anabala Hezironi; ndi Hezironi anabala Ramu; |
Chewa Bible 2014 |
|
1 |
BUKU la kubadwa kwa Yesu Kristu, mwana wa Davide, mwana wa Abrahamu. |
2 |
Abrahamu anabala Isake; ndi Isake anabala Yakobo; ndi Yakobo anabala Yuda ndi abale ace; |
3 |
ndi Yuda anabala Farese ndi Zara mwa Tamare; ndi Farese anabala Ezronu; ndi Ezronu anabala Aramu; |
Chewa Bible (BL) 1992 |
|